kusonkhanitsa okhulupilira 1 million kuti akaf- ikire

6
KUSONKHANITSA OKHULUPILIRA 1 MILLION KUTI AKAF- IKIRE ANTHU 1 BILLION NDI UTHENGA WABWINO TIYENI TONSE TITENGEPO MBALI! YENSE WOKHULUPILIRA NDI MBONI YA UTHENGA WABWINO – TONSE PAMODZI TITHA KUFIKIRA DZIKO LONSE LAPANSI!

Upload: others

Post on 11-Apr-2022

2 views

Category:

Documents


0 download

TRANSCRIPT

Page 1: KUSONKHANITSA OKHULUPILIRA 1 MILLION KUTI AKAF- IKIRE

KUSONKHANITSA OKHULUPILIRA 1 MILLION KUTI AKAF-IKIRE ANTHU 1 BILLION NDI UTHENGA WABWINOTIYENI TONSE TITENGEPO MBALI!

YENSE WOKHULUPILIRA NDI MBONI YA UTHENGA WABWINO – TONSE PAMODZI TITHA KUFIKIRA DZIKO LONSE LAPANSI!

Page 2: KUSONKHANITSA OKHULUPILIRA 1 MILLION KUTI AKAF- IKIRE

GOALS MALAWI: • Mobilizing at least 12.000 Christians from at least

480 Churches to reach 1.080.000 people with the Gospel.

• Disciple and incorporate at least 540, 000 new believers into exis-ting Churches.

• Every church growing by 10% as a result of Go 2020.

<<invitation text>>

<<web url>>

<<theProblem1>>

<<theProblem2>>

93%

Tikukuitanirani kuti mukhale otengapo mbali pomodzi ndi mipingo ndi mautumiki achuluka pa dziko lonse lapansi ndi kugwiritsa ntchito mwezi onse wa Meyi 2020 pola-likira uthenga wabwino wa Yesu Khristu. Tangoganizirani m'mene ichi chingakhudzire anthu ozungulira dela, m’mzinda ndi dziko lonse lapansi!

www.go2020.world | www.globaloutreachday.com

“Pomwepo ananena kwa ophunzira ace, zotuta zicurukadi koma anchito ali oweren-geka” Mateyu 9:37

Pa anthu 100 alionse 93 mu mpingo satha kuchitira umboni za chikhulupiliro chawo ndi ena. Izi zitha kusinthidwa!

93%

Page 3: KUSONKHANITSA OKHULUPILIRA 1 MILLION KUTI AKAF- IKIRE

KODI MUNGATENGE NAWO MBALI MOTANI?Pemphelani limodzi ndi mazana mazana a Akhristu mu Sabata yoyambilila ya mwenzi wa Meyi. Chitani mitundu yonse yofalitsira Uthenga wa bwino mu mwenzi onse wa Meyi

OKHULUPILILA WINA ALIYENSE ANTHA KUFIKIRA ANTHU ASANU

Gawanani Uthenga wa Bwino ndi anzanu, amene aku-zungulirani kudela kwanu, ogwira nawo ntchito ndi amubanja mwanu. Chonde satirani malangizo a boma popewa Kolona Vailasi (matenda a COVID 19) potalikirana ndi anzanu. Pempherelani ndi kusamalira osowa. Uzani ena za Uthenga wa bwino kuzera mu masamba a intaneti, mafoni, polemberana kalata monga imelo komanso ngati nzotheka poyankhulana. Umboni wanu utha kusintha mioyo kwa muyaya!

MPINGO ULIWONSE UTHA KUKONZA ZOCHITIKA ZOCHITIRA UMBONI

Potalikirana muthakuuza ena za Uthenga wa Bwino pokwiritsa ntchito makina a intaneti ndi mumagulu ang'ono-ang'ono. Njira imeneyi itha kugwiritsidwanso ntchito pophunzitsa ena za chikhulupiriro, potumiza ma uthenga olimbikitsa ena ndikuthandiza ena. Gwiritsani ntchito njira zilizonse malingana ndi mumene zithu zilili kudela kwanu pofotokozera ena za Uthenga wa Bwino.

MASABATA ASANU AMWEZI WA MEYI 2020

Page 4: KUSONKHANITSA OKHULUPILIRA 1 MILLION KUTI AKAF- IKIRE

ZAKA ZISANU NDI MPHAMBU ZITATU ZOFIKIRA DZIKOLONSE NDI UTHENGA WABWINO

• Anthu okhulupilira 25 million anachitira um-boni za chikhulupililo chawo, ambiri mwaiwo kanali koyamba kuchitira umboni chibadwire.

• Anthu oponsela 10 Million anapulumutsidwa. • Mazana mazana a magulu a anthu okhulupi-

rira • Munamtindi obatizidwa ku Caribbean

Zodabwitsa! Chifukwa cha tsiku lofalitsa Uthenga wa bwino pa dziko lonse lapansi, mipingo yanthu yokwana 300 inakula ndi anthu okwana 2,300. Panopa ambiri ayife timatuluka kukafalitsa Uthenga wa bwino.Pastor Marcio F. Barboza CesarRio Grande do Sul, Brasil

PEMPHELERANI kupulumutsidwa kwa anthu ochuluka. SONKHANITSANI ndi KUPHUNZIT-SA anthu za kuchitira umboni za utheka wab-wino. Gwiritsani ntchito kabuku ka “Masitepe Atatu” kopezeka pa tsamba la intaneti ili www.go2020.world

Simukuyenela kudikira paka mu Meyi. Yamba-ni kuchitira umboni ndi kukhazikitsa zochitika zochitira umboni. Chonde dziwitsani azibusa ena ndi mipingo idziwe za Mwezi ochitira um-boni mu 2020.

PHUNZITSANI anthu onse amene atem-benuka mtima ndi kuwalandira mu mpingo wanu, yambani magulu ang’ono-ang’ono ndi kubzala mipingo.

KUPITIRIZA KUFALITSA Pitilizani kuchitira umboni:: - Mwenzi uliwonse kapena sabata iliyonse ngati mpingo.

- Sabata iliyonse kapena tsiku lililonse ngati wokhulupilira.

Kuyambira pa 31 Okutobala pakana pa 1 Novemba 2020: Batizani okhulupirira onse musabata yaubatizo padziko lonse lapansi

Mu Sabata yoyamba ya Meyi: Pemphe-rani limodzi ndi okhulupilira 100 million, tumizani mpingo wanu kukachitira umboni.

Mwezi wa Meyi: Njira zonse zochitira umboni, makamaka pogwiritsa ntchito njira zina zamakonozamakono, zalamya ndi intaneti

Pa 30 Meyi 2020: Okhulupilira wina aliyense ndi mipingo idzala-rikira uthenga wabwino pa tsiku limeneli lofikira dziko lonse ndi uthenga wa Yesu Khristu

TISANAFIKE MU MEYI

MU MWEZI WA MEYI 2020

TIKATHA MWENZI WA MEYI

ZOCHITIKA

Page 5: KUSONKHANITSA OKHULUPILIRA 1 MILLION KUTI AKAF- IKIRE

CHIYEMBEKEZO KUCHOTSA MANTHADziko lino liri pamavuto chifukwa cha muliri wa Kolona. Anthu ambiri ali ndi mantha ndipo akufunafuna mayankho. Panopa kuposa kale pakusowekera kutukulira anthu kwa ambuye powapempherera, kuwathandizira muzosowa zawo ndi kugawana nawo Uthenga wa Bwino.

PempheroPempherani kuti Mulungu alowerere munyengo ino ya mulili wa Korona komanso kuti anthu ambiri atembenuke mitima mu mwezi wa Meyi 2020.

Kufalitsa UthengaMipingo yokwana 1 million ndi okhulupilila okwana 100 million akhala akuchitira umboni za Uthenga wabwino mu mwezi wa Meyi.

MaguluZonyezani ZIZINDIKIRO ZINAYI pamasamba a intaneti kapena popanga zionetsero zazizindiki-ro ndi gulu la anthu ena ngati zingatheke.

Kuphunzitsa (Kupanga Ophunzira)Anthu amene atembenuka mtima aphunzitsidwe ndi kukhazikitsidwa mu mipingo.

KusamaliraSamalirani anthu osowa ndi amene ali mumavuto. Mutha kuonetsera umodzi wanu powathandiza iwo ndizithu zofunikira pamoyo wawo wa tsiku ndi tsiku..

KubatizidwaThawi ya kumapeto kwa Sabata yomaliza ya mwenzi wa Okutobala 2020 mazana a anthu amene atembenuka mtima adzakala akuba-tizidwa.

Mwezi ochitira umboni uthandizira mpingo wanu kuti ukule ndi chikhalidwe chatsopano chochitira umboni za uthenga wabwino.

Page 6: KUSONKHANITSA OKHULUPILIRA 1 MILLION KUTI AKAF- IKIRE

KUYANKHULANA MALAWI National CoordinatorTimothy Zimba +265 888 38 29 [email protected]

National Vice-CoordinatorGerald Khowani+265 888 89 56 [email protected]

Ziwani zambiri pa tsamba la intaneti www.go2020.worldPezani ka buku ka “Masitepe Atatu” ndi zida zina zompunzitsira. Lembetsani dzina la mpingo wanu ndi kupereka cholinga chanu.

Tsiku lochitira umboni pa dziko lonse ndi njira yabwino yolimbikitsa anthu kuti ayambe kugawana ndi ena za Chikhupiri chawo.Steve Douglass, Mutsogoleri Campus Crusade for Christ (Life Ministry)

Uthenga wabwino ndi uthenga okhawo woposa wina uliwonse ndipo tonsefe tinai-tanidwa kuti tikaufalitse, ndikuthana ndi chete wa ChiKhristu! Lingalilani za mwenzi wochitira umboni ndi zotsatira zake ngati okhulupirira wina aliyense atakhala woten-gapo mbali.

Werner Nachtigal, Mutsogoleri wa Global Outreach Day

Chonde ziwitsani azibusa, mipingo ndi okhulupilira onse

za Mwezi wochitira umboni Uthenga wa bwino wa Khristu

TIYENI TONSE TITENGEPO!

Tauzani ena za umboni wanu wa chipulumutso pa tsam-

ba a intaneti la #globaloutreach #go2020

GLOBAL OUTREACH DAY

3STEPSIN PERSONAL EVANGELISM

TRAINING BOOK

Werner Nachtigal

GLOBAL OUTREACH DAY

3STEPSIN PERSONAL EVANGELISM

TRAINING BOOK

Werner Nachtigal

GLOBAL OUTREACH DAY

3STEPSIN PERSONAL EVANGELISM

TRAINING BOOK

Werner Nachtigal

MWEZI OCHITIRA UMBONI ndi mbali yapadela ya TSIKU LOCHITIRA UMBONI PA DZIKO LONSE LAPANSI

ABALE MU UTUMIKI

…ndi ena ambiri

Tsiku lochitira Umboni pa dziko lonse lapansi ndi masophenya ochoka kwa Mulungu. Ndikugawana nanu masom-phenya amenewa kuti dziko lililonse lifikiridwe ndi uthenga wabwino.Loren Cunningham, Uyambitsa bungwe la YWAM

Mwezi wochitira umboni ndi mwayi wa okhulupirira onse pa dziko lonse lapansi kuti amuke ndi kukachitira umboni wa Yesu Khristu. Ndikupepha wina aliyense kuti tipite ndikukafalitsa unthenga wachipulumutso.Bishop Efraim Tendero, World Evangelical Alliance